Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 33:51 - Buku Lopatulika

51 Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Mutaoloka Yordani kulowa m'dziko la Kanani,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

51 Nena ndi ana a Israele, nuti nao, Mutaoloka Yordani kulowa m'dziko la Kanani,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

51 “Uza Aisraele kuti, Pamene muwoloka mtsinje wa Yordani kuti muloŵe m'dziko la Kanani,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

51 “Nena kwa Aisraeli kuti, ‘Pamene muwoloka Yorodani kulowa mʼdziko la Kanaani,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 33:51
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Yehova ananena ndi Mose m'zidikha za Mowabu pa Yordani ku Yeriko, nati,


Pamene Yehova Mulungu wanu atakulowetsani m'dziko limene munkako kulilandira likhale lanulanu, ndipo atakataya amitundu ambiri pamaso panu, Ahiti, ndi Agirigasi, ndi Aamori, ndi Akanani, ndi Aperizi, ndi Ahivi, ndi Ayebusi, mitundu isanu ndi iwiri yaikulu ndi yamphamvu yoposa inu;


Imvani Israele; mulikuoloka Yordani lero lino, kulowa ndi kulandira amitundu akulu ndi amphamvu akuposa inu, mizinda yaikulu ndi ya malinga ofikira kuthambo,


Ndipo ansembe akulisenza likasa la chipangano la Yehova, anaima pouma pakati pa Yordani, ndi Aisraele onse anaoloka pouma mpaka mtundu wonse unatha kuoloka Yordani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa