Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 33:32 - Buku Lopatulika

32 Nachokera ku Bene-Yaakani, nayenda namanga mu Hori Hagidigadi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

32 Nachokera ku Bene-Yaakani, nayenda namanga m'Hori Hagidigadi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

32 Adanyamuka ku Beneyakana, nakamanga mahema ao ku Horo-Hagidigadi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

32 Atachoka ku Beni Yaakani anakamanga ku Hori-Hagidigadi.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 33:32
6 Mawu Ofanana  

Ana a Ezere ndi awa: Bilihani, ndi Zaavani, ndi Akani.


Ana a Ezere: Bilihani, ndi Zaavani, ndi Yaakani. Ana a Disani: Uzi, ndi Arani.


Nachokera ku Meseroti, nayenda namanga mu Bene-Yaakani.


Nachokera ku Hori Hagidigadi, nayenda namanga mu Yotibata.


Ndipo ana a Israele anayenda ulendo wao kuchokera ku zitsime za ana a Yaakani kufikira ku Mosera. Kumeneko anamwalira Aroni, ndi kumeneko anamuika; ndipo Eleazara mwana wake anachita ntchito ya nsembe m'malo mwake.


Kuchokerako ananka ulendo ku Gudigoda, ndi kuchokera ku Gudigoda kunka ku Yotibata, dziko la mitsinje yamadzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa