Numeri 33:30 - Buku Lopatulika30 Nachokera ku Hasimona, nayenda namanga mu Meseroti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Nachokera ku Hasimona, nayenda namanga m'Meseroti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Adanyamuka ku Hasimona, nakamanga mahema ao ku Meseroti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Atachoka ku Hasimona anakamanga ku Moseroti. Onani mutuwo |