Numeri 33:29 - Buku Lopatulika29 Nachokera ku Mitika, nayenda namanga mu Hasimona. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Nachokera ku Mitika, nayenda namanga m'Hasimona. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Adanyamuka ku Mitika, nakamanga mahema ao ku Hasimona. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Atachoka ku Mitika anakamanga ku Hasimona. Onani mutuwo |