Numeri 32:36 - Buku Lopatulika36 ndi Betenimura, ndi Beteharani: mizinda ya m'malinga, ndi makola a zoweta. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 ndi Betenimura, ndi Beteharani: midzi ya m'malinga, ndi makola a zoweta. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Betenimira ndi Beteharani. Yonseyo inali yozingidwa ndi malinga. Ndipo adamanganso makola a nkhosa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Beti-Nimira ndi Beti-Harani mizinda ya malinga. Anamanganso makola a ziweto zawo. Onani mutuwo |