Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 32:28 - Buku Lopatulika

28 Pamenepo Mose anamuuza Eleazara wansembe, ndi Yoswa mwana wa Nuni, ndi akulu a makolo a mafuko a ana a Israele za iwo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

28 Pamenepo Mose anamuuza Eleazara wansembe, ndi Yoswa mwana wa Nuni, ndi akulu a makolo a mafuko a ana a Israele za iwo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

28 Choncho Mose adalamula wansembe Eleazara, Yoswa mwana wa Nuni, ndi atsogoleri a mabanja a mafuko a Aisraele kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

28 Choncho Mose anapereka malamulo awa kwa wansembe Eliezara, kwa Yoswa mwana wa Nuni ndi kwa akulu a mafuko a Aisraeli.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 32:28
3 Mawu Ofanana  

koma anyamata anu adzaoloka, yense wokonzekera ndi zankhondo pamaso pa Yehova kunkhondo, monga wanena mbuyanga.


Ndipo Mose anati kwa iwo, Ngati ana a Gadi ndi ana a Rubeni aoloka nanu Yordani, yense wokonzekera ndi zankhondo pamaso pa Yehova, ndi dziko lagonjera inu; pamenepo muwapatse dziko la Giliyadi likhale laolao;


Kumbukirani mau amene Mose mtumiki wa Yehova anakulamulirani inu, kuti, Yehova Mulungu wanu akupatsani mpumulo, nadzakupatsani dziko lino.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa