Numeri 31:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo anawathira nkhondo Amidiyani, monga Yehova adamuuza Mose; nawapha amuna onse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo anawathira nkhondo Amidiyani, monga Yehova adamuuza Mose; nawapha amuna onse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Aisraelewo adamenyana nkhondo ndi Amidiyani, monga momwe Chauta adaalamulira Mose, ndipo adapha amuna onse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Iwo anamenyana ndi Amidiyani monga momwe Yehova analamulira Mose ndipo anapha mwamuna aliyense. Onani mutuwo |