Numeri 31:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo anapereka mwa zikwi za Israele, a fuko limodzi chikwi chimodzi, anthu zikwi khumi ndi ziwiri okonzekeratu ndi zankhondo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo anapereka mwa zikwi za Israele, a fuko limodzi chikwi chimodzi, anthu zikwi khumi ndi ziwiri okonzekeratu ndi zankhondo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Choncho pa anthu a Aisraele ambirimbiri aja, Mose adatumiza anthu chikwi chimodzi pa fuko lililonse, ndipo onse anali 12,000 pamodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Choncho amuna okwana 12,000 anatenga zida kukonzekera nkhondo, anthu 1,000 kuchokera ku fuko lililonse la Aisraeli. Onani mutuwo |