Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 31:32 - Buku Lopatulika

32 Ndipo zakunkhondo, zotsalira zofunkha zonse adazifunkha ankhondowa, ndizo nkhosa zikwi mazana asanu ndi limodzi mphambu zikwi makumi asanu ndi awiri kudza zisanu,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

32 Ndipo zakunkhondo, zotsalira zofunkha zonse adazifunkha ankhondowa, ndizo nkhosa zikwi mazana asanu ndi limodzi mphambu zikwi makumi asanu ndi awiri kudza zisanu,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

32 Zofunkha zotsala zimene ankhondowo adalanda zinali izi: nkhosa 675,000,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

32 Zotsala pa zolanda ku nkhondo zimene ankhondowo anatenga zinali nkhosa 675,000,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 31:32
4 Mawu Ofanana  

Zoweta zakenso zinali nkhosa zikwi zisanu ndi ziwiri, ndi ngamira zikwi zitatu, ndi ng'ombe zamagoli mazana asanu, ndi abulu aakazi mazana asanu, antchito ake omwe ndi ambiri; chotero munthuyu anaposa anthu onse a kum'mawa.


Ndipo Mose ndi Eleazara wansembe anachita monga Yehova anamuuza Mose.


ndi ng'ombe zikwi makumi asanu ndi awiri mphambu ziwiri,


Popeza wankhondo yense anadzifunkhira yekha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa