Numeri 31:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo Mose ananena ndi anthu, nati, Adzikonzere ena mwa inu zida za nkhondo, alimbane nao Amidiyani, kuwabwezera Amidiyani chilango cha Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo Mose ananena ndi anthu, nati, Adzikonzere ena mwa inu zida za nkhondo, alimbane nao Amidiyani, kuwabwezera Amidiyani chilango cha Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mose adauza Aisraele kuti, “Amuna ena pakati panupa mutenge zida zankhondo, kuti mukamenyane ndi Amidiyani, kuti Chauta aŵalipsire. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ndipo Mose anati kwa Aisraeli, “Perekani zida kwa ena mwa anthu anu kuti akamenyane ndi Amidiyani ndi kuwabwezera choyipa mʼmalo mwa Yehova. Onani mutuwo |