Numeri 31:26 - Buku Lopatulika26 Werengani zakunkhondo, ndizo anthu, ndi zoweta, iwe, ndi Eleazara wansembe, ndi akulu a nyumba za makolo za khamulo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Werengani zakunkhondo, ndizo anthu, ndi zoweta, iwe, ndi Eleazara wansembe, ndi akulu a nyumba za makolo za khamulo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 “Iwe, ndi wansembe Eleazara, pamodzi ndi atsogoleri a mabanja a mpingo, muŵerenge zofunkha zimene adalanda pa nkhondo, anthu pamodzi ndi nyama zomwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 “Iwe ndi wansembe Eliezara ndiponso akuluakulu a mabanja a anthuwa, muwerenge anthu onse ndi ziweto zomwe zinagwidwa ku nkhondo. Onani mutuwo |