Numeri 31:27 - Buku Lopatulika27 nugawe zakunkhondo pawiri; pakati pa othira nkhondo amene anatuluka kunkhondo, ndi khamu lonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 nugawe zakunkhondo pawiri; pakati pa othira nkhondo amene anatuluka kunkhondo, ndi khamu lonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Ndipo mugaŵe zofunkhazo magawo aŵiri, lina la ankhondo amene adaapita ku nkhondo, lina la mpingo wonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Mugawe zolanda ku nkhondozo magawo awiri, lina la ankhondo amene anapita ku nkhondo, lina la anthu onse. Onani mutuwo |