Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 31:24 - Buku Lopatulika

24 Ndipo mutsuke zovala zanu tsiku lachisanu ndi chiwiri, kuti mukhale oyera; ndipo mutatero mulowe m'chigono.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Ndipo muzitsuke zovala zanu tsiku lachisanu ndi chiwiri, kuti mukhale oyera; ndipo mutatero mulowe m'chigono.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Muchape zovala zanu pa tsiku lachisanu ndi chiŵiri, ndipo mudzayeretsedwa. Pambuyo pake muloŵe ku mahema.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Pa tsiku lachisanu ndi chiwiri muchape zovala zanu ndipo mudzayera. Mukatero mutha kulowa mu msasa.”

Onani mutuwo Koperani




Numeri 31:24
6 Mawu Ofanana  

ndipo aliyense akanyamulako nyama ya mtembo wake azitsuka zovala zake, nadzakhala wodetsedwa kufikira madzulo.


Ndipo tsiku lachisanu ndi chiwiri kudzakhala kuti amete tsitsi lake lonse la pamutu pake, ndi ndevu zake, ndi nsidze zake, inde amete tsitsi lake lonse; natsuke zovala zake, nasambe thupi lake ndi madzi, nakhale woyera.


Ndipo wakukhayo atayeretsedwa ku kukha kwake, adziwerengere masiku asanu ndi awiri akhale a kuyeretsa kwake, natsuke zovala zake; nasambe thupi lake ndi madzi oyenda, nadzakhala woyera.


Ndipo woyerayo awaze pa wodetsedwayo tsiku lachitatu, ndi tsiku lachisanu ndi chiwiri; ndipo tsiku lachisanu ndi chiwiri amyeretse; ndipo atsuke zovala zake, nasambe m'madzi, nadzakhala woyera madzulo.


zonse zakulola moto, mupititse m'moto, ndipo zidzakhala zoyera; koma muziyeretsenso ndi madzi akusiyanitsa. Koma zonse zosalola moto, muzipititse m'madzi.


Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa