Numeri 3:35 - Buku Lopatulika35 Ndi kalonga wa nyumba ya makolo ya mabanja la Merari ndiye Zuriyele mwana wa Abihaili; azimanga mahema ao pa mbali ya chihema cha kumpoto. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Ndi kalonga wa nyumba ya makolo ya mabanja la Merari ndiye Zuriyele mwana wa Abihaili; azimanga mahema ao pa mbali ya Kachisi ya kumpoto. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Ndipo munthu amene anali mutu wa mabanja a Merari anali Zuriyele mwana wa Abihaili. Iwo ankamanga zithando zao kumpoto kwa chihema cha Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Mtsogoleri wa magulu a mabanja a Amerari anali Zuriyeli mwana wa Abihaili. Iwo ankamanga misasa yawo kumpoto kwa Chihema. Onani mutuwo |