Numeri 29:26 - Buku Lopatulika26 Ndi tsiku lachisanu ng'ombe zisanu ndi zinai, nkhosa zamphongo ziwiri, anaankhosa khumi ndi anai, a chaka chimodzi, opanda chilema; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndi tsiku lachisanu ng'ombe zisanu ndi zinai, nkhosa zamphongo ziwiri, anaankhosa khumi ndi anai, a chaka chimodzi, opanda chilema; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 “Pa tsiku lachisanu mupereke ng'ombe zisanu ndi zinai zamphongo, nkhosa ziŵiri zamphongo, anaankhosa khumi ndi anai amphongo a chaka chimodzi opanda chilema, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 “ ‘Pa tsiku lachisanu muzipereka ngʼombe zazimuna zisanu ndi zinayi, nkhosa zazimuna ziwiri ndi ana ankhosa aamuna khumi ndi anayi a chaka chimodzi, zonse zopanda chilema. Onani mutuwo |