Numeri 29:15 - Buku Lopatulika15 ndi limodzi la magawo khumi likhale la mwanawankhosa mmodzi, momwemo nao anaankhosa khumi ndi anai; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 ndi limodzi la magawo khumi likhale la mwanawankhosa mmodzi, momwemo nao anaankhosa khumi ndi anai; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 ndi wa kilogaramu limodzi pa mwanawankhosa aliyense. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Pa mwana wankhosa aliyense mwa ana ankhosa aamuna khumi ndi anayiwo, muzipereka chakudya cha kilogalamu imodzi. Onani mutuwo |