Numeri 28:29 - Buku Lopatulika29 limodzi la magawo khumi likhale la mwanawankhosa mmodzi, momwemo ndi anaankhosa asanu ndi awiri; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 limodzi la magawo khumi likhale la mwanawankhosa mmodzi, momwemo ndi anaankhosa asanu ndi awiri; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 ndiponso wa kilogaramu limodzi pa mwanawankhosa aliyense. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Ndipo pa mwana wankhosa aliyense mwa asanu ndi awiri aja, kilogalamu imodzi. Onani mutuwo |