Numeri 28:18 - Buku Lopatulika18 Tsiku loyamba pali kusonkhana kopatulika; musamachita ntchito ya masiku ena; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Tsiku loyamba pali kusonkhana kopatulika; musamachita ntchito ya masiku ena; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Pa tsiku loyamba pazikhala msonkhano wopatulika. Musagwire ntchito yotopetsa, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Pa tsiku loyamba muzichita msonkhano wopatulika ndipo musamagwire ntchito iliyonse. Onani mutuwo |