Numeri 28:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo mwezi woyamba, tsiku lakhumi ndi chinai la mwezi pali Paska wa Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo mwezi woyamba, tsiku lakhumi ndi chinai la mwezi pali Paska wa Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 “Tsiku la 14 la mwezi woyamba, ndi la Paska ya Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 “ ‘Pa tsiku la 14 la mwezi woyamba muzichita Paska wa Yehova. Onani mutuwo |