Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 27:22 - Buku Lopatulika

22 Ndipo Mose anachita monga Yehova adamuuza; natenga Yoswa namuimitsa pamaso pa Eleazara wansembe, ndi pamaso pa khamu lonse;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Ndipo Mose anachita monga Yehova adamuuza; natenga Yoswa namuimitsa pamaso pa Eleazara wansembe, ndi pamaso pa khamu lonse;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Mose adachitadi monga momwe Chauta adamlamulira. Adamtengadi Yoswa namuimiritsa pamaso pa wansembe Eleazara ndi pamaso pa mpingo wonse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Mose anachita monga Yehova anamulamulira. Anatenga Yoswa ndi kumuyimiritsa pamaso pa Eliezara wansembe ndi pamaso pa gulu lonse.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 27:22
3 Mawu Ofanana  

Ndipo ana a Aroni ndiwo Eleazara mwana wake, Finehasi mwana wake, Abisuwa mwana wake,


Ndipo aime pamaso pa Eleazara wansembe, amene amfunsire monga mwa chiweruzo cha Urimu pamaso pa Yehova; ponena iye azituluka, ndi ponena iye azilowa, ndi iye ndi ana onse a Israele pamodzi naye, ndiwo khamu lonse.


namuikira manja ake, namlangiza monga Yehova adanena ndi dzanja la Mose.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa