Numeri 27:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Kwera m'phiri ili la Abarimu, nupenye dziko limene ndapatsa ana a Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo Yehova anati kwa Mose, Kwera m'phiri ili la Abarimu, nupenye dziko limene ndapatsa ana a Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Chauta adauza Mose kuti, “Ukwere phiri ili la Abarimu, kuti uwone dziko limene ndapatsa Aisraele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Kenaka Yehova anati kwa Mose, “Kwera phiri la Abarimu kuti ukaone dziko limene ndalipereka kwa Aisraeli. Onani mutuwo |