Numeri 25:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo Mose anati kwa oweruza a Israele, Iphani, yense anthu ake adaphatikanawo ndi Baala-Peori. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo Mose anati kwa oweruza a Israele, Iphani, yense anthu ake adaphatikanawo ndi Baala-Peori. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Apo Mose adauza oweruza a Aisraele kuti, “Aliyense mwa inu aphe anthu ake amene adapembedza nao Baala wa ku Peori.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Choncho Mose anawuza oweruza a Israeli kuti, “Aliyense wa inu ayenera kupha anthu ake amene anapembedza nawo Baala-Peori.” Onani mutuwo |