Numeri 24:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo ananena fanizo lake, nati, Balamu mwana wa Beori anenetsa, ndi munthu wotsinzina masoyo anenetsa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo ananena fanizo lake, nati, Balamu mwana wa Beori anenetsa, ndi munthu wotsinzina masoyo anenetsa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Ndipo adayambapo kulankhula mau auneneri adati, “Mau a Balamu mwana wa Beori, mau a munthu amene maso ake ndi otsekuka, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Ndipo iye ananena uthenga wake nati, “Uthenga wa Balaamu mwana wa Beori, uthenga wa amene diso lake ndi lotsekuka. Onani mutuwo |