Numeri 23:28 - Buku Lopatulika28 Ndipo Balaki ananka naye Balamu pamwamba pa Peori, popenyana ndi chipululu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndipo Balaki ananka naye Balamu pamwamba pa Peori, popenyana ndi chipululu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Choncho Balaki adatenga Balamu, napita naye pamwamba pa phiri la Peori loyang'anana ndi chipululu cham'munsi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Ndipo Balaki anamutengera Balaamu pamwamba pa Peori, poyangʼanana ndi chipululu. Onani mutuwo |