Numeri 23:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo ananena fanizo lake, nati, Ukani, Balaki, imvani; ndimvereni, mwana wa Zipori. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo ananena fanizo lake, nati, Ukani, Balaki, imvani; ndimvereni, mwana wa Zipori. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Apo Balamu adayamba kulankhula mau auneneri, adati, “Dzukani, Balaki, ndipo mumve, mundimvere inu mwana wa Zipori. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Pamenepo Balaamu ananena uthenga wake: “Nyamuka Balaki ndipo tamvera; Undimvere iwe mwana wa Zipori. Onani mutuwo |