Numeri 22:36 - Buku Lopatulika36 Pamene Balaki anamva kuti wafika Balamu, anamtulukira kukakomana naye kumzinda wa Mowabu, wokhala m'mphepete mwa Arinoni, ndiwo ku malekezero a malire ake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Pamene Balaki anamva kuti wafika Balamu, anamtulukira kukakomana naye kumudzi wa Mowabu, wokhala m'mphepete mwa Arinoni, ndiwo ku malekezero a malire ake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Balaki atamva kuti Balamu wafika, adatuluka kukamchingamira ku mzinda wina wokhala pafupi ndi mtsinje wa Arinoni, umene umachita malire a dziko la Mowabu, kumapeto kwake kwenikweni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Balaki atamva kuti Balaamu akubwera, anapita kukakumana naye ku mzinda wa Mowabu umene unali mʼmalire a Arinoni, mʼmphepete mwa dziko lake. Onani mutuwo |