Numeri 22:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo bulu anati kwa Balamu, Si ndine bulu wako amene umayenda wokwera pa ine chiyambire ndili wako kufikira lero lino? Kodi ndikakuchitira chotere ndi kale lonse? Ndipo anati, Iai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo bulu anati kwa Balamu, Si ndine bulu wako amene umayenda wokwera pa ine chiyambire ndili wako kufikira lero lino? Kodi ndikakuchitira chotere ndi kale lonse? Ndipo anati, Iai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Buluyo adafunsanso Balamu kuti, “Kodi sindine bulu wanu amene mwakhala mukundikwera moyo wanu wonse mpaka lero lino? Kodi zimenezi ndidakuchitiranipo nkale lonse?” Balamu adayankha kuti “Iyai.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Buluyo anati kwa Balaamu, “Kodi sindine bulu wanu, amene mumakwera nthawi zonse kufikira lero? Kodi ndinakuchitiranipo zoterezi?” Iye anati “Ayi.” Onani mutuwo |