Numeri 22:21 - Buku Lopatulika21 Pamenepo Balamu anauka m'mawa namanga bulu wake, namuka nao akalonga a ku Mowabu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Pamenepo Balamu anauka m'mawa namanga bulu wake, namuka nao akalonga a ku Mowabu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Choncho Balamu, atadzuka m'maŵa mwake, adaika chishalo pa bulu wake, ndipo adanyamuka pamodzi ndi akalonga aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Balaamu anadzuka mmawa, namanga bulu wake wamkazi ndipo anapita ndi akuluakulu a Mowabu. Onani mutuwo |