Numeri 21:27 - Buku Lopatulika27 Chifukwa chake iwo akunena mophiphiritsa akuti, Idzani ku Hesiboni, mzinda wa Sihoni umangike, nukhazikike. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Chifukwa chake iwo akunena mophiphiritsa akuti, Idzani ku Hesiboni, mudzi wa Sihoni umangike, nukhazikike. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Nchifukwa chake oimba ndakatulo amati, “Bwerani ku Hesiboni, mzindawu umangidwenso, tiyeni timange mzinda wa Sihoni kuti ukhazikikenso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Nʼchifukwa chake alakatuli amati: “Bwerani ku Hesiboni, mzindawo umangidwenso; mzinda wa Sihoni ukhazikike. Onani mutuwo |