Numeri 20:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Mose ndi Aroni anachoka pamaso pa msonkhano kunka ku khomo la chihema chokomanako, nagwa nkhope zao pansi; ndipo ulemerero wa Yehova unaonekera iwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Mose ndi Aroni anachoka pamaso pa msonkhano kunka ku khomo la chihema chokomanako, nagwa nkhope zao pansi; ndipo ulemerero wa Yehova unaonekera iwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Apo Mose ndi Aroni adachoka pa msonkhano uja, napita ku khomo la chihema chamsonkhano, ndipo adadziponya pansi. Pomwepo ulemerero wa Chauta udaŵaonekera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Mose ndi Aaroni anachoka mu msonkhano ndi kupita pa khomo la tenti ya msonkhano, nagwa pansi chafufumimba ndipo ulemerero wa Yehova unaonekera. Onani mutuwo |