Numeri 19:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo chilichonse munthu wodetsedwa achikhudza chidzakhala chodetsedwa; ndi munthu wakuchikhudza adzakhala wodetsedwa kufikira madzulo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo chilichonse munthu wodetsedwa achikhudza chidzakhala chodetsedwa; ndi munthu wakuchikhudza adzakhala wodetsedwa kufikira madzulo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Chinthu chilichonse chimene munthu woipitsidwa akhudza, chidzakhala choipitsidwa. Ndipo munthu aliyense wokhudza chimenecho, adzakhala woipitsidwa mpaka madzulo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Chilichonse chimene munthu wodetsedwayo achikhudze chidzakhala chodetsedwa ndiponso aliyense wochikhudza adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.” Onani mutuwo |