Numeri 19:20 - Buku Lopatulika20 Koma munthu wakukhala wodetsedwa, koma wosadziyeretsa, azimsadza munthuyo pakati pa msonkhano, popeza waipsa malo opatulika a Yehova; sanamwaze madzi akusiyanitsa; ndiye wodetsedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Koma munthu wakukhala wodetsedwa, koma wosadziyeretsa, azimsadza munthuyo pakati pa msonkhano, popeza waipsa malo opatulika a Yehova; sanamwaze madzi akusiyanitsa; ndiye wodetsedwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 “Koma munthu woipitsidwa akapanda kudziyeretsa, ameneyo achotsedwe pakati pa msonkhano, pakuti waipitsa malo opatulika a Chauta. Ameneyo ndi woipitsidwa chifukwa sadamuwaze madzi oyeretsera aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Koma ngati munthu wodetsedwayo sadziyeretsa yekha, ndiye kuti ayenera kuchotsedwa pakati pa gulu chifukwa anadetsa malo wopatulika a Yehova, popeza sanawazidwe madzi oyeretsa ndiye kuti ndi wodetsedwa. Onani mutuwo |