Numeri 18:29 - Buku Lopatulika29 Mupereke nsembe zokweza zonse za Yehova kuzitenga ku mphatso zanu zonse, kusankhako zokometsetsa ndizo zopatulika zake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Mupereke nsembe zokweza zonse za Yehova kuzitenga ku mphatso zanu zonse, kusankhako zokometsetsa ndizo zopatulika zake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Pa mphatso zonse zimene mwalandira, mupatuleko zake za Chauta, ndipo zimene mwapatulazo zikhale zabwino kopambana zina zonse.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Muyenera kupereka monga gawo la Yehova magawo abwino kwambiri ndi opatulika a chilichonse chimene chapatsidwa kwa inu.’ Onani mutuwo |