Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 17:9 - Buku Lopatulika

9 Ndipo Mose anatulutsa ndodo zonse kuzichotsa pamaso pa Yehova, azione ana onse a Israele; ndipo anapenya, natenga yense ndodo yake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndipo Mose anatulutsa ndodo zonse kuzichotsa pamaso pa Yehova, azione ana onse a Israele; ndipo anapenya, natenga yense ndodo yake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Tsono Mose adatulutsa ndodo zonse zija pamaso pa Chauta ndi kuŵaonetsa Aisraele. Ataona, mtsogoleri aliyense adatenga ndodo yake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Choncho Mose anatulutsa ndodo zonse pamaso pa Yehova napita nazo kwa Aisraeli onse. Iwowo anaziona ndipo munthu aliyense anatenga ndodo yake.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 17:9
2 Mawu Ofanana  

Ndipo Yehova anati kwa Mose, Bweza ndodo ya Aroni kuiika chakuno cha mboni, isungike ikhale chizindikiro cha pa ana opikisana; kuti unditsirizire madandaulo ao, kuti ungafe.


Ndipo kunali m'mawa mwake, kuti Mose analowa m'chihema cha mboni; ndipo taonani, ndodo ya Aroni, ya pa banja la Levi, inaphuka, n'kutulutsa timaani, ndi kuchita maluwa, n'kubereka akatungurume.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa