Numeri 17:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Mose ananena ndi ana a Israele, ndipo akalonga ao onse anapereka, yense ndodo imodzi, monga mwa mabanja a makolo ao, ndodo khumi ndi ziwiri; ndi ndodo ya Aroni inakhala pakati pa ndodo zao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Mose ananena ndi ana a Israele, ndipo akalonga ao onse anapereka, yense ndodo imodzi, monga mwa mabanja a makolo ao, ndodo khumi ndi ziwiri; ndi ndodo ya Aroni inakhala pakati pa ndodo zao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Choncho Mose adalankhula ndi Aisraele. Ndipo atsogoleri onse adampatsa ndodozo, mtsogoleri aliyense ndodo imodzi molingana ndi mafuko a makolo ao, ndiye kuti ndodo khumi ndi ziŵiri pamodzi. Ndodo ya Aroni inali pakati pa ndodo zao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Choncho Mose anayankhula ndi Aisraeli, ndipo atsogoleri awo anapereka ndodo khumi ndi ziwiri, imodzi kuchokera kwa mtsogoleri wa fuko lililonse ndipo ndodo ya Aaroni inali pakati pa ndodo zawozo. Onani mutuwo |