Numeri 16:45 - Buku Lopatulika45 Kwerani kuchoka pakati pa khamu lino, kuti ndiwathe m'kamphindi. Pamenepo adagwa nkhope zao pansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201445 Kwerani kuchoka pakati pa khamu lino, kuti ndiwathe m'kamphindi. Pamenepo adagwa nkhope zao pansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa45 “Choka pakati pa gulu la anthuli, kuti ndiŵaononge onse nthaŵi imodzi.” Aŵiriwo adadziponya pansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero45 “Chokani pakati pa gulu la anthuwa kuti ndiwawononge kamodzinʼkamodzi.” Ndipo iwo anagwa pansi chafufumimba. Onani mutuwo |