Numeri 16:43 - Buku Lopatulika43 Ndipo Mose ndi Aroni anadza kukhomo kwa chihema chokomanako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 Ndipo Mose ndi Aroni anadza kukhomo kwa chihema chokomanako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 Mose ndi Aroni adabwera patsogolo pa chihema chamsonkhano, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 Pamenepo Mose ndi Aaroni anapita patsogolo pa tenti ya msonkhano ija Onani mutuwo |