Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 16:34 - Buku Lopatulika

34 Ndipo Aisraele onse akukhala pozinga pao anathawa pakumva kufuula kwao; pakuti anati, Lingatimeze dziko ifenso.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

34 Ndipo Aisraele onse akukhala pozinga pao anathawa pakumva kufuula kwao; pakuti anati, Lingatimeze dziko ifenso.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

34 Pomwepo Aisraele onse amene anali pafupi adathaŵa, atamva anthuwo akulira. Ankati, “Tiyeni tithaŵe kuti nthakayi ingatimeze nafenso.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

34 Atamva kulira kwawo, Aisraeli onse amene anali pafupi ndi anthuwo anathawa akufuwula kuti, “Nthaka imezanso ife!”

Onani mutuwo Koperani




Numeri 16:34
6 Mawu Ofanana  

Pa mau a phokoso mitundu ya anthu yathawa; ponyamuka iwe amitundu abalalika.


Pamenepo mudzathawa kudzera chigwa cha mapiri anga; pakuti chigwa cha mapiri chidzafikira ku Azali; ndipo mudzathawa monga umo munathawira chivomezi, masiku a Uziya mfumu ya Yuda; ndipo Yehova Mulungu wanga adzadza, ndi opatulika onse pamodzi ndi Inu.


Chomwecho iwowa, ndi onse anali nao, anatsikira kumanda ali ndi moyo, ndi dziko linasunama pa iwo, ndipo anaonongeka pakati pa msonkhano.


Ndipo moto unatuluka kwa Yehova, ndi kunyeketsa amuna mazana awiri ndi makumi asanu aja akubwera nacho chofukiza.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa