Numeri 16:24 - Buku Lopatulika24 Nena ndi khamulo, ndi kuti, Kwerani kuchoka pozungulira mahema a Kora, Datani, ndi Abiramu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Nena ndi khamulo, ndi kuti, Kwerani kuchoka pozungulira mahema a Kora, Datani, ndi Abiramu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 “Uza mpingo kuti achoke pafupi ndi mahema a Kora, Datani ndi Abiramu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 “Uza gulu lonse kuti, ‘Khalani kutali ndi matenti a Kora, Datani ndi Abiramu.’ ” Onani mutuwo |