Numeri 16:14 - Buku Lopatulika14 Ndiponso sunatilowetse m'dziko moyenda mkaka ndi uchi ngati madzi, kapena kutipatsa cholowa cha minda, ndi minda yampesa; kodi udzakolowola amuna awa maso ao: Sitifikako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndiponso sunatilowetsa m'dziko moyenda mkaka ndi uchi ngati madzi, kapena kutipatsa cholowa cha minda, ndi minda yamphesa; kodi udzakolowola amuna awa maso ao: Sitifikako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Kuwonjezera apo, simudatiloŵetse m'dziko lamwanaalirenji, ndipo simudatipatse polima kapena minda yamphesa, kuti ikhale choloŵa chathu. Kodi mukufuna kutigwira m'maso? Ife sitibwera kumeneko.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Kuwonjezera apo, sunatilowetse mʼdziko loyenda mkaka ndi uchi kapena kutipatsa malo wolima ndi minda ya mpesa. Kodi ukufuna kuchotsa maso a anthuwa? Ayi, sitibwera!” Onani mutuwo |