Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 15:41 - Buku Lopatulika

41 Ine ndine Yehova Mulungu wanu, wakukutulutsani m'dziko la Ejipito, kuti ndikhale Mulungu wanu; Ine ndine Yehova Mulungu wanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

41 Ine ndine Yehova Mulungu wanu, wakukutulutsani m'dziko la Ejipito, kuti ndikhale Mulungu wanu; Ine ndine Yehova Mulungu wanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

41 Ine ndine Chauta amene ndidakutulutsani ku dziko la Ejipito, kuti ndikhale Mulungu wanu. Ine ndine Chauta.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

41 Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani mʼdziko la Igupto kuti ndikhale Mulungu wanu. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.’ ”

Onani mutuwo Koperani




Numeri 15:41
11 Mawu Ofanana  

Kuti asamalire malemba ake, nasunge malamulo ake. Aleluya.


ndipo ndidzalandira inu mukhale anthu anga, ndipo ndidzakhala Ine Mulungu wanu; ndipo mudzadziwa kuti Ine ndine Yehova Mulungu wanu, wakutulutsa inu pansi pa akatundu a Aejipito.


amene ndinakutulutsani m'dziko la Ejipito, kuti ndikhale Mulungu wanu; Ine ndine Yehova.


Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani m'dziko la Ejipito, kukupatsani dziko la Kanani, kuti ndikhale Mulungu wanu.


kuti mukumbukire ndi kuchita malamulo anga onse, ndi kukhala wopatulikira Mulungu wanu.


Koma Kora, mwana wa Izihara, mwana wa Kohati, mwana wa Levi, anatenga Datani ndi Abiramu, ana a Eliyabu, ndi Oni mwana wa Peleti, ana a Rubeni;


Koma tsopano akhumba lina loposa, ndilo la mu Mwamba; mwa ichi Mulungu sachita manyazi nao poitanidwa Mulungu wao; pakuti adawakonzera mzinda.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa