Numeri 14:8 - Buku Lopatulika8 Yehova akakondwera nafe, adzatilowetsa m'dzikomo, ndi kutipatsa ilo; ndilo dziko moyenda mkaka ndi uchi ngati madzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Yehova akakondwera nafe, adzatilowetsa m'dzikomo, ndi kutipatsa ilo; ndilo dziko moyenda mkaka ndi uchi ngati madzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Ngati Chauta amatikonda, adzatiloŵetsa m'dziko lamwanaalirenjilo ndi kutipatsa kuti likhale lathu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Ngati Yehova akukondwera nafe, adzatitsogolera kulowa mʼdziko limenelo. Dziko loyenda mkaka ndi uchi adzalipereka kwa ife, Onani mutuwo |