Numeri 13:31 - Buku Lopatulika31 Koma anthu adakwera nayewo anati, Sitingathe kuwakwerera anthuwo; popeza atiposa mphamvu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Koma anthu adakwera nayewo anati, Sitikhoza kuwakwerera anthuwo; popeza atiposa mphamvu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Tsono anthu aja amene adaapita naye limodziŵa adati, “Sitingathe kukalimbana nawo anthuwo, poti ngamphamvu kopambana ife.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Koma anthu aja amene anapita naye anati, “Sitingathe kulimbana ndi anthuwo popeza ndi amphamvu kuposa ifeyo.” Onani mutuwo |