Numeri 12:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo atatero anthuwo ananka ulendo wao kuchokera ku Hazeroti, namanga mahema ao m'chipululu cha Parani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo atatero anthuwo ananka ulendo wao kuchokera ku Hazeroti, namanga mahema ao m'chipululu cha Parani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Pambuyo pake anthu aja adanyamuka ku Hazeroti nakamanga mahema ao ku chipululu cha Parani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Pambuyo pake anthu ananyamuka ku Heziroti ndi kukamanga mʼchipululu cha Parani. Onani mutuwo |