Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 12:15 - Buku Lopatulika

15 Pamenepo anambindikiritsa Miriyamu kunja kwa chigono masiku asanu ndi awiri; ndipo anthu sanayende ulendo kufikira atamlandiranso Miriyamu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Pamenepo anambindikiritsa Miriyamu kunja kwa chigono masiku asanu ndi awiri; ndipo anthu sanayende ulendo kufikira atamlandiranso Miriyamu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Choncho adamtsekera Miriyamu kunja kwa mahema masiku asanu ndi aŵiri. Ndipo anthu sadathe kunyamuka ulendo wao mpaka Miriyamu atamloŵetsanso.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Choncho anamutsekera Miriamu kunja kwa msasa masiku asanu ndi awiri ndipo anthu sanayende ulendo wawo mpaka Miriamu atamulowetsanso.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 12:15
9 Mawu Ofanana  

Uzilemekeza atate wako ndi amai ako; kuti achuluke masiku ako m'dziko limene Yehova Mulungu wako akupatsa iwe.


Angakhale aliritsa, koma adzachitira chisoni monga mwa kuchuluka kwa zifundo zake.


Ndipo iye wakuti ayeretsedwe atsuke zovala zake, namete tsitsi lake lonse, nasambe madzi, nakhale woyera; ndipo atatero alowe kuchigono, koma agone pa bwalo la hema wake masiku asanu ndi awiri.


Pakuti ndinakukwezani kukutulutsani m'dziko la Ejipito, ndi kuombola inu m'nyumba ya ukapolo; ndipo ndinatuma akutsogolereni Mose, Aroni, ndi Miriyamu.


Yehova, ndinamva mbiri yanu ndi mantha; Yehova, tsitsimutsani ntchito yanu pakati pa zaka, pakati pa zaka mudziwitse; pa mkwiyo mukumbukire chifundo.


Ndipo atatero anthuwo ananka ulendo wao kuchokera ku Hazeroti, namanga mahema ao m'chipululu cha Parani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa