Numeri 11:28 - Buku Lopatulika28 Ndipo Yoswa mwana wa Nuni, mtumiki wa Mose kuyambira ubwana wake, anayankha nati, Mose, mfumu yanga, aletseni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndipo Yoswa mwana wa Nuni, mtumiki wa Mose kuyambira ubwana wake, anayankha nati, Mose, mfumu yanga, aletseni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Apo Yoswa, mwana wa Nuni, mtumiki wa Mose, mmodzi mwa anthu ake osankhidwa aja, adati, “Mbuyanga Mose, aletseni amenewo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Yoswa mwana wa Nuni, mtumiki wa Mose kuyambira ubwana wake, anayankha kuti, “Mbuye wanga Mose, aletseni!” Onani mutuwo |