Numeri 11:19 - Buku Lopatulika19 Simudzadya tsiku limodzi, kapena masiku awiri, kapena masiku asanu, kapena masiku khumi, kapena masiku makumi awiri; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Simudzadya tsiku limodzi, kapena masiku awiri, kapena masiku asanu, kapena masiku khumi, kapena masiku makumi awiri; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Simudzaidya tsiku limodzi lokha, kapena masiku aŵiri okha, kapena masiku asanu okha, kapena masiku khumi okha, kapena masiku makumi aŵiri okha ai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Simudzadya tsiku limodzi lokha, kapena masiku awiri, kapena asanu, khumi kapena masiku makumi awiri, Onani mutuwo |