Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 1:49 - Buku Lopatulika

49 Fuko la Levi lokha usaliwerenge, kapena kuona kufikira kwao mwa ana a Israele;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

49 Fuko la Levi lokha usaliwerenge, kapena kuona kufikira kwao mwa ana a Israele;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

49 “Fuko la Levi usaliŵerenge ai, anthu ake usaŵalembere kumodzi ndi Aisraele enawo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

49 “Usawerenge fuko la Levi kapena kuliphatikiza mʼkawundula wa Aisraeli.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 1:49
3 Mawu Ofanana  

Popeza Yehova adalankhula ndi Mose, ndi kuti,


Koma sanawerenge Alevi mwa ana a Israele; monga Yehova adauza Mose.


Ndipo owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi awiri mphambu zitatu, mwamuna yense wa mwezi umodzi ndi mphambu; popeza sanawerengedwe pakati pa ana a Israele; chifukwa sanawapatse cholowa mwa ana a Israele.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa