Numeri 1:25 - Buku Lopatulika25 owerengedwa ao a fuko la Gadi, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu kudza mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 owerengedwa ao a fuko la Gadi, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu kudza mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Tsono ataŵerenga maina onse a m'fuko la Gadi, adapezeka kuti ali 45,650. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Gadi chinali 45, 650. Onani mutuwo |