Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 1:25 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Chiwerengero cha anthu ochokera mʼfuko la Gadi chinali 45, 650.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

25 owerengedwa ao a fuko la Gadi, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu kudza mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 owerengedwa ao a fuko la Gadi, ndiwo zikwi makumi anai mphambu zisanu kudza mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Tsono ataŵerenga maina onse a m'fuko la Gadi, adapezeka kuti ali 45,650.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 1:25
4 Mawu Ofanana  

Kuchokera mwa zidzukulu za Gadi: Amuna onse a zaka makumi awiri kapena kupitirirapo, omwe akanatha kugwira ntchito ya usilikali anawalemba mayina awo monga mwa mbiri ya mafuko awo ndi mabanja awo.


Kuchokera mwa zidzukulu za Yuda: Amuna onse a zaka makumi awiri kapena kupitirirapo, omwe akanatha kugwira ntchito ya usilikali anawalemba mayina awo monga mwa mbiri ya mafuko awo ndi mabanja awo.


Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 45,650.


Awa ndiwo anali mafuko a Gadi. Onse amene anawerengedwa analipo 40,500.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa